Machitidwe 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chotero tikutumiza Yudasi ndi Sila,+ kuti iwonso adzakufotokozereni zinthu zomwezi mwa mawu apakamwa.+ 2 Atesalonika 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo, pamene ndili limodzi ndi Silivano ndi Timoteyo,+ ndikulembera mpingo wa Atesalonika wogwirizana ndi Mulungu Atate wathu, ndi Ambuye Yesu Khristu, kuti: 1 Petulo 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndakulemberani m’mawu ochepa kudzera mwa Silivano,+ m’bale amene ndikumuona kuti ndi wokhulupirika. Ndakulemberani zimenezi+ kuti ndikulimbikitseni ndi kupereka umboni wamphamvu wakuti kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu n’kumeneku, ndipo mukugwire mwamphamvu.+
27 Chotero tikutumiza Yudasi ndi Sila,+ kuti iwonso adzakufotokozereni zinthu zomwezi mwa mawu apakamwa.+
1 Ine Paulo, pamene ndili limodzi ndi Silivano ndi Timoteyo,+ ndikulembera mpingo wa Atesalonika wogwirizana ndi Mulungu Atate wathu, ndi Ambuye Yesu Khristu, kuti:
12 Ndakulemberani m’mawu ochepa kudzera mwa Silivano,+ m’bale amene ndikumuona kuti ndi wokhulupirika. Ndakulemberani zimenezi+ kuti ndikulimbikitseni ndi kupereka umboni wamphamvu wakuti kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu n’kumeneku, ndipo mukugwire mwamphamvu.+