Machitidwe 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chilamulo ndi Zolemba za aneneri zitawerengedwa pamaso pa anthu,+ atsogoleri+ a sunagoge anawatumizira mawu akuti: “Amuna inu, abale athu, ngati muli ndi mawu alionse olimbikitsa nawo anthu, lankhulani.” Machitidwe 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atakhala kumeneko kwa kanthawi, ananyamuka ndi kuyenda malo osiyanasiyana m’chigawo cha Galatiya+ ndi Fulugiya,+ ndipo anali kulimbikitsa+ ophunzira onse.
15 Chilamulo ndi Zolemba za aneneri zitawerengedwa pamaso pa anthu,+ atsogoleri+ a sunagoge anawatumizira mawu akuti: “Amuna inu, abale athu, ngati muli ndi mawu alionse olimbikitsa nawo anthu, lankhulani.”
23 Atakhala kumeneko kwa kanthawi, ananyamuka ndi kuyenda malo osiyanasiyana m’chigawo cha Galatiya+ ndi Fulugiya,+ ndipo anali kulimbikitsa+ ophunzira onse.