Numeri 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Mose anapanga njoka yamkuwa+ ndi kuiika pamtengo wachizindikirowo.+ Ndipo zinachitikadi kuti munthu akalumidwa ndi njoka n’kuyang’ana+ njoka yamkuwayo, anali kukhalabe ndi moyo.+ Deuteronomo 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndidzawapatsa mneneri ngati iwe kuchokera pakati pa abale awo.+ Ndidzaika mawu anga m’kamwa mwake,+ ndipo adzawauza zonse zimene ndidzamulamula.+
9 Pamenepo Mose anapanga njoka yamkuwa+ ndi kuiika pamtengo wachizindikirowo.+ Ndipo zinachitikadi kuti munthu akalumidwa ndi njoka n’kuyang’ana+ njoka yamkuwayo, anali kukhalabe ndi moyo.+
18 Ndidzawapatsa mneneri ngati iwe kuchokera pakati pa abale awo.+ Ndidzaika mawu anga m’kamwa mwake,+ ndipo adzawauza zonse zimene ndidzamulamula.+