Genesis 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamene Abulamu anali ndi zaka 99, Yehova anaonekera kwa iye n’kumuuza kuti:+ “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Yenda pamaso panga ndipo ukhale wolungama.+ Genesis 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Muzichita mdulidwe kuti ukhale chizindikiro cha pangano la pakati pa ine ndi inu.+ Machitidwe 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Anamupatsanso pangano la mdulidwe.+ Chotero anabereka Isaki+ ndi kuchita mdulidwe wake tsiku la 8.+ Isaki naye anabereka Yakobo, Yakobo anabereka mitu ya mabanja 12 ija.+
17 Pamene Abulamu anali ndi zaka 99, Yehova anaonekera kwa iye n’kumuuza kuti:+ “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Yenda pamaso panga ndipo ukhale wolungama.+
8 “Anamupatsanso pangano la mdulidwe.+ Chotero anabereka Isaki+ ndi kuchita mdulidwe wake tsiku la 8.+ Isaki naye anabereka Yakobo, Yakobo anabereka mitu ya mabanja 12 ija.+