Danieli 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Ndiyeno iwe pita ku mapeto+ ndipo udzapuma.+ Koma udzauka kuti ulandire gawo lako pa mapeto a masikuwo.”+ Luka 20:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma zakuti akufa amaukitsidwa ngakhalenso Mose anafotokoza m’nkhani ya chitsamba cha minga.+ M’nkhani imeneyo iye ananena kuti Yehova ndi ‘Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo.’+ Aefeso 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiponso, Mulungu anapangitsa inuyo kukhala amoyo pamene munali akufa chifukwa cha zolakwa zanu ndi machimo anu.+ Aheberi 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma anadziwa kuti Mulungu ali ndi mphamvu zomuukitsa kwa akufa.+ Ndipo iye anamulandiradi kuchokera kwa akufa m’njira ya fanizo.+
13 “Ndiyeno iwe pita ku mapeto+ ndipo udzapuma.+ Koma udzauka kuti ulandire gawo lako pa mapeto a masikuwo.”+
37 Koma zakuti akufa amaukitsidwa ngakhalenso Mose anafotokoza m’nkhani ya chitsamba cha minga.+ M’nkhani imeneyo iye ananena kuti Yehova ndi ‘Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo.’+
2 Ndiponso, Mulungu anapangitsa inuyo kukhala amoyo pamene munali akufa chifukwa cha zolakwa zanu ndi machimo anu.+
19 Koma anadziwa kuti Mulungu ali ndi mphamvu zomuukitsa kwa akufa.+ Ndipo iye anamulandiradi kuchokera kwa akufa m’njira ya fanizo.+