Luka 20:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Iye ndi Mulungu wa anthu amoyo, osati akufa, pakuti kwa iye onsewa ndi amoyo.”+ 1 Akorinto 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mulungu anasankha zinthu zonyozeka za dziko ndi zinthu zimene anthu amaziona ngati zachabechabe, zinthu zimene palibe,+ kuti athetse+ mphamvu zinthu zimene zilipo, 1 Petulo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti kale simunali mtundu, koma tsopano ndinu mtundu wa anthu a Mulungu.+ Munali anthu amene sanakuchitireni chifundo, koma tsopano ndinu amene mwachitiridwa chifundo.+
28 Mulungu anasankha zinthu zonyozeka za dziko ndi zinthu zimene anthu amaziona ngati zachabechabe, zinthu zimene palibe,+ kuti athetse+ mphamvu zinthu zimene zilipo,
10 Pakuti kale simunali mtundu, koma tsopano ndinu mtundu wa anthu a Mulungu.+ Munali anthu amene sanakuchitireni chifundo, koma tsopano ndinu amene mwachitiridwa chifundo.+