Machitidwe 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mulungu wa makolo athu anaukitsa+ Yesu, amene inu munamupha mwa kumupachika pamtengo.+ 2 Akorinto 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anaferanso onse kuti amene ali moyo asakhale moyo wongodzisangalatsa okha,+ koma akhale moyo wosangalatsa amene anawafera+ n’kuukitsidwa.+
15 Iye anaferanso onse kuti amene ali moyo asakhale moyo wongodzisangalatsa okha,+ koma akhale moyo wosangalatsa amene anawafera+ n’kuukitsidwa.+