Aroma 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kwenikweni, Chilamulo chimabala mkwiyo,+ koma pamene palibe lamulo, palibenso kulakwa.+ Aroma 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chilamulo+ chinalowapo kuti kuchimwa kuonekere kuti ndi kwakukulu.+ Koma pamene uchimo+ unawonjezeka, kukoma mtima kwakukulu+ kunasefukiranso.
20 Chilamulo+ chinalowapo kuti kuchimwa kuonekere kuti ndi kwakukulu.+ Koma pamene uchimo+ unawonjezeka, kukoma mtima kwakukulu+ kunasefukiranso.