Yohane 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chobadwa mwa thupi n’chanyama, ndipo chobadwa mwa mzimu n’chauzimu.+ Agalatiya 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano, ntchito za thupi zimaonekera.+ Ntchitozi ndizo dama,*+ zinthu zodetsa, khalidwe lotayirira,+
19 Tsopano, ntchito za thupi zimaonekera.+ Ntchitozi ndizo dama,*+ zinthu zodetsa, khalidwe lotayirira,+