Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 29:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Anthu inu ndinu opotoka maganizo kwabasi! Kodi woumba zinthu ndi dongo angafanane ndi dongolo?+ Kodi chinthu chochita kupangidwa chingamunene amene anachipanga, kuti: “Iye uja sanandipange”?+ Komanso kodi chinthu chochita kuumbidwa chingamunene amene anachiumba, kuti: “Iye uja sanasonyeze kuti ndi womvetsa zinthu”?+

  • Yesaya 45:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Tsoka kwa amene walimbana ndi amene anamuumba,+ ngati phale limene likulimbana ndi mapale ena amene ali pansi. Kodi dongo+ lingafunse amene akuliumba kuti: “Kodi ukupanga chiyani?” Ndipo kodi chimene unapanga chinganene kuti: “Amene uja alibe manja”?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena