Yohane 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Mawu ameneyo anakhala ndi thupi+ la nyama ndi kukhala pakati pathu, ndipo tinaona ulemerero wake, ulemerero wa mwana wobadwa yekha+ kwa bambo ake. Anali wodzaza ndi kukoma mtima kwakukulu ndi choonadi.+ Agalatiya 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma nthawi itakwana,+ Mulungu anatumiza Mwana wake,+ amene anadzabadwa kwa mkazi+ ndipo anadzakhala pansi pa chilamulo.+
14 Choncho Mawu ameneyo anakhala ndi thupi+ la nyama ndi kukhala pakati pathu, ndipo tinaona ulemerero wake, ulemerero wa mwana wobadwa yekha+ kwa bambo ake. Anali wodzaza ndi kukoma mtima kwakukulu ndi choonadi.+
4 Koma nthawi itakwana,+ Mulungu anatumiza Mwana wake,+ amene anadzabadwa kwa mkazi+ ndipo anadzakhala pansi pa chilamulo.+