1 Akorinto 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi sindine mfulu?+ Kodi sindine mtumwi?+ Kodi sindinaone Yesu Ambuye wathu?+ Kodi inu sindinu ntchito yanga mwa Ambuye? 1 Akorinto 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ineyo ndine wamng’ono kwambiri+ mwa atumwi onse, ndipo si ine woyenera kutchedwa mtumwi, chifukwa ndinazunza+ mpingo wa Mulungu.
9 Kodi sindine mfulu?+ Kodi sindine mtumwi?+ Kodi sindinaone Yesu Ambuye wathu?+ Kodi inu sindinu ntchito yanga mwa Ambuye?
9 Ineyo ndine wamng’ono kwambiri+ mwa atumwi onse, ndipo si ine woyenera kutchedwa mtumwi, chifukwa ndinazunza+ mpingo wa Mulungu.