2 Akorinto 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndithudi inuyo munaona umboni wakuti ndine mtumwi,+ poona mmene ndinapiririra,+ komanso poona zizindikiro, zodabwitsa, ndi ntchito zamphamvu zimene ndinachita.+ 1 Timoteyo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa cha umboni umenewu,+ ine ndinasankhidwa kuti ndikhale mlaliki ndi mtumwi.+ Ndikunenatu zoona,+ sindikunama ayi. Ndinasankhidwa kuti ndikhale mphunzitsi wophunzitsa anthu a mitundu ina+ za chikhulupiriro+ ndi choonadi.
12 Ndithudi inuyo munaona umboni wakuti ndine mtumwi,+ poona mmene ndinapiririra,+ komanso poona zizindikiro, zodabwitsa, ndi ntchito zamphamvu zimene ndinachita.+
7 Chifukwa cha umboni umenewu,+ ine ndinasankhidwa kuti ndikhale mlaliki ndi mtumwi.+ Ndikunenatu zoona,+ sindikunama ayi. Ndinasankhidwa kuti ndikhale mphunzitsi wophunzitsa anthu a mitundu ina+ za chikhulupiriro+ ndi choonadi.