Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 28:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Anali kuwalalikira za ufumu wa Mulungu ndi kuwaphunzitsa za Ambuye Yesu Khristu, mwaufulu wonse wa kulankhula+ popanda choletsa.

  • Akolose 1:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Adzaterodi, malinga ngati mupitirizabe m’chikhulupiriro,+ muli okhazikika pamaziko+ ndiponso olimba, osasunthika+ pa chiyembekezo cha uthenga wabwino umene munamva,+ umenenso unalalikidwa+ m’chilengedwe chonse+ cha pansi pa thambo. Uthenga wabwino umenewu ndi umene ineyo Paulo ndinakhala mtumiki wake.+

  • 1 Timoteyo 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndikuyamika Khristu Yesu Ambuye wathu amene anandipatsa mphamvu poona kuti ndine wokhulupirika,+ ndipo anandipatsa utumiki.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena