Aroma 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene amadya, asanyoze amene sadya,+ ndipo wosadyayo asaweruze amene amadya, popeza ameneyo analandiridwa ndi Mulungu. 1 Akorinto 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zikatero, ungawononge munthu wofookayo, yemwe ndi m’bale wako amene Khristu anamufera,+ chifukwa chakuti ukudziwa zinthu.
3 Amene amadya, asanyoze amene sadya,+ ndipo wosadyayo asaweruze amene amadya, popeza ameneyo analandiridwa ndi Mulungu.
11 Zikatero, ungawononge munthu wofookayo, yemwe ndi m’bale wako amene Khristu anamufera,+ chifukwa chakuti ukudziwa zinthu.