Aroma 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma sindikufuna kuti mukhale osadziwa abale,+ kuti nthawi zambiri ndinkafuna kubwera kwanuko,+ koma pakhala zondilepheretsa mpaka pano. Ndikufuna kuti ndidzapeze zipatso+ pakati pa inu monganso ndinachitira pakati pa mitundu ina yonse.
13 Koma sindikufuna kuti mukhale osadziwa abale,+ kuti nthawi zambiri ndinkafuna kubwera kwanuko,+ koma pakhala zondilepheretsa mpaka pano. Ndikufuna kuti ndidzapeze zipatso+ pakati pa inu monganso ndinachitira pakati pa mitundu ina yonse.