Machitidwe 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Ayuda anafika kuchokera ku Antiokeya ndi ku Ikoniyo ndipo anakopa anthuwo.+ Choncho anaponya Paulo miyala ndi kumukokera kunja kwa mzindawo, poganiza kuti wafa.+ Machitidwe 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atamva zimenezi Hananiya mkulu wa ansembe, analamula anthu amene anaimirira pafupi naye kuti amubwanyule+ pakamwa. 2 Akorinto 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kasanu Ayuda anandikwapula zikoti 40+ kuchotsera chimodzi.
19 Ndiyeno Ayuda anafika kuchokera ku Antiokeya ndi ku Ikoniyo ndipo anakopa anthuwo.+ Choncho anaponya Paulo miyala ndi kumukokera kunja kwa mzindawo, poganiza kuti wafa.+
2 Atamva zimenezi Hananiya mkulu wa ansembe, analamula anthu amene anaimirira pafupi naye kuti amubwanyule+ pakamwa.