1 Timoteyo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Asakhale wotembenuka kumene,+ kuopera kuti angakhale wotukumuka chifukwa cha kunyada,+ n’kulandira chiweruzo chofanana ndi chimene Mdyerekezi analandira.+
6 Asakhale wotembenuka kumene,+ kuopera kuti angakhale wotukumuka chifukwa cha kunyada,+ n’kulandira chiweruzo chofanana ndi chimene Mdyerekezi analandira.+