Yohane 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 kuti onsewa akhale amodzi,+ mmene inu Atate ndi ine tilili ogwirizana,+ kuti iwonso akhale ogwirizana ndi ife,+ ndi kuti dziko likhulupirire kuti inu munanditumadi.+ 1 Yohane 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zimene taziona ndi kuzimva, tikukuuzani+ kuti inunso mugwirizane nafe.+ Ndipotu, ifeyo ndife ogwirizana+ ndi Atate ndi Mwana wake Yesu Khristu.+
21 kuti onsewa akhale amodzi,+ mmene inu Atate ndi ine tilili ogwirizana,+ kuti iwonso akhale ogwirizana ndi ife,+ ndi kuti dziko likhulupirire kuti inu munanditumadi.+
3 Zimene taziona ndi kuzimva, tikukuuzani+ kuti inunso mugwirizane nafe.+ Ndipotu, ifeyo ndife ogwirizana+ ndi Atate ndi Mwana wake Yesu Khristu.+