Aroma 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+ 1 Akorinto 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+ Aefeso 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti mfundo iyi mukuidziwa, ndipo mukuimvetsa bwino, kuti wadama+ kapena wodetsedwa kapena waumbombo,+ umene ndiwo kupembedza mafano, sadzalowa mu ufumu wa Khristu ndi wa Mulungu.+
28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+
9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+
5 Pakuti mfundo iyi mukuidziwa, ndipo mukuimvetsa bwino, kuti wadama+ kapena wodetsedwa kapena waumbombo,+ umene ndiwo kupembedza mafano, sadzalowa mu ufumu wa Khristu ndi wa Mulungu.+