Maliko 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo iye anayamba kuwauza kuti: “Inu mwapatsidwa mwayi wozindikira chinsinsi chopatulika+ cha ufumu wa Mulungu. Koma kwa amene ali kunja zonse zimachitika mwa mafanizo,+
11 Ndipo iye anayamba kuwauza kuti: “Inu mwapatsidwa mwayi wozindikira chinsinsi chopatulika+ cha ufumu wa Mulungu. Koma kwa amene ali kunja zonse zimachitika mwa mafanizo,+