1 Akorinto 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ineyo pandekha, ngakhale kuti mwa thupi sindili kumeneko koma mu mzimu ndili komweko, ndamuweruza kale+ ndithu munthu amene wachita zimenezi, ngati kuti ndinali nanu kumeneko. Tito 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 wogwira mwamphamvu mawu okhulupirika pamene akuphunzitsa mwaluso,+ kuti athe kulimbikitsa anthu ndi chiphunzitso cholondola+ ndiponso kudzudzula+ otsutsa. Aheberi 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Muzimvera amene akutsogolera pakati panu+ ndipo muziwagonjera.+ Iwo amayang’anira miyoyo yanu monga anthu amene adzayankhe mlandu.+ Muziwamvera ndi kuwagonjera kuti agwire ntchito yawo mwachimwemwe, osati modandaula, pakuti akatero zingakhale zokuvulazani.+
3 Ineyo pandekha, ngakhale kuti mwa thupi sindili kumeneko koma mu mzimu ndili komweko, ndamuweruza kale+ ndithu munthu amene wachita zimenezi, ngati kuti ndinali nanu kumeneko.
9 wogwira mwamphamvu mawu okhulupirika pamene akuphunzitsa mwaluso,+ kuti athe kulimbikitsa anthu ndi chiphunzitso cholondola+ ndiponso kudzudzula+ otsutsa.
17 Muzimvera amene akutsogolera pakati panu+ ndipo muziwagonjera.+ Iwo amayang’anira miyoyo yanu monga anthu amene adzayankhe mlandu.+ Muziwamvera ndi kuwagonjera kuti agwire ntchito yawo mwachimwemwe, osati modandaula, pakuti akatero zingakhale zokuvulazani.+