Numeri 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Malo amenewo anawatcha Kibiroti-hatava,+ chifukwa anafotserapo anthu amene anasonyeza mtima wadyera.+ Salimo 106:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anasonyeza chikhumbo chawo chadyera m’chipululu,+Ndipo anayesa Mulungu m’chipululumo.+
34 Malo amenewo anawatcha Kibiroti-hatava,+ chifukwa anafotserapo anthu amene anasonyeza mtima wadyera.+