Aroma 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho, tiyeni titsatire zinthu zobweretsa mtendere+ ndiponso zolimbikitsana.+ Aroma 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aliyense wa ife azikondweretsa mnzake pa zinthu zabwino zomulimbikitsa.+