Machitidwe 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atatero anamugwira dzanja lake lamanja+ ndi kumuimiritsa. Nthawi yomweyo kunsi kwa mapazi ake komanso mafupa ake a akakolo zinalimba.+ Machitidwe 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Izi zitachitika, anthu ena onse pachilumbacho amene anali kudwala, nawonso anabwera kwa iye ndipo anawachiritsa.+
7 Atatero anamugwira dzanja lake lamanja+ ndi kumuimiritsa. Nthawi yomweyo kunsi kwa mapazi ake komanso mafupa ake a akakolo zinalimba.+
9 Izi zitachitika, anthu ena onse pachilumbacho amene anali kudwala, nawonso anabwera kwa iye ndipo anawachiritsa.+