Machitidwe 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano mumpingo wa ku Antiokeya munali aneneri+ ndi aphunzitsi. Iwo anali Baranaba, Sumeoni wotchedwa Nigeri, Lukiyo+ wa ku Kurene, Manayeni amene anaphunzira pamodzi ndi Herode wolamulira chigawo, ndi Saulo. Aefeso 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo anapereka ena monga atumwi,+ ena monga aneneri,+ ena monga alaliki,*+ ena monga abusa ndi aphunzitsi,+
13 Tsopano mumpingo wa ku Antiokeya munali aneneri+ ndi aphunzitsi. Iwo anali Baranaba, Sumeoni wotchedwa Nigeri, Lukiyo+ wa ku Kurene, Manayeni amene anaphunzira pamodzi ndi Herode wolamulira chigawo, ndi Saulo.
11 Ndipo anapereka ena monga atumwi,+ ena monga aneneri,+ ena monga alaliki,*+ ena monga abusa ndi aphunzitsi,+