Aroma 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwa ameneyunso, ndiponso chifukwa cha chikhulupiriro, takhala ndi ufulu wolowa+ m’kukoma mtima kwakukulu, mmene tilimo tsopano. Ndipo tiyeni tikondwere chifukwa cha chiyembekezo+ cha ulemerero wa Mulungu.
2 Mwa ameneyunso, ndiponso chifukwa cha chikhulupiriro, takhala ndi ufulu wolowa+ m’kukoma mtima kwakukulu, mmene tilimo tsopano. Ndipo tiyeni tikondwere chifukwa cha chiyembekezo+ cha ulemerero wa Mulungu.