Afilipi 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero, ngati pakati panu pali kulimbikitsana kulikonse mwa Khristu,+ kaya kutonthozana kulikonse kwa chikondi, kaya mzimu woganizirana,+ kaya chikondi chachikulu+ chilichonse ndi chifundo, 2 Atesalonika 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso, Ambuye wathu Yesu Khristu mwiniyo, ndi Mulungu Atate wathu, amene anatikonda+ ndipo amatilimbikitsa m’njira yosalephera ndiponso anatipatsa chiyembekezo chabwino,+ mwa kukoma mtima kwakukulu,
2 Chotero, ngati pakati panu pali kulimbikitsana kulikonse mwa Khristu,+ kaya kutonthozana kulikonse kwa chikondi, kaya mzimu woganizirana,+ kaya chikondi chachikulu+ chilichonse ndi chifundo,
16 Komanso, Ambuye wathu Yesu Khristu mwiniyo, ndi Mulungu Atate wathu, amene anatikonda+ ndipo amatilimbikitsa m’njira yosalephera ndiponso anatipatsa chiyembekezo chabwino,+ mwa kukoma mtima kwakukulu,