Afilipi 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mulungu ndiye mboni yanga kuti ndikufunitsitsa nditakuonani nonsenu. Ndikufunitsitsa nditakuonani ndi chikondi chachikulu+ ngati chimene Khristu Yesu ali nacho. Akolose 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero monga ochita kusankhidwa ndi Mulungu,+ oyera ndi okondedwa, valani chifundo+ chachikulu, kukoma mtima, kudzichepetsa,+ kufatsa,+ ndi kuleza mtima.+ 1 Petulo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano, popeza mwayeretsa+ miyoyo yanu mwa kukhala omvera choonadi ndipo zotsatira zake n’zakuti mumakonda abale mopanda chinyengo,+ kondanani kwambiri kuchokera mumtima.+
8 Mulungu ndiye mboni yanga kuti ndikufunitsitsa nditakuonani nonsenu. Ndikufunitsitsa nditakuonani ndi chikondi chachikulu+ ngati chimene Khristu Yesu ali nacho.
12 Chotero monga ochita kusankhidwa ndi Mulungu,+ oyera ndi okondedwa, valani chifundo+ chachikulu, kukoma mtima, kudzichepetsa,+ kufatsa,+ ndi kuleza mtima.+
22 Tsopano, popeza mwayeretsa+ miyoyo yanu mwa kukhala omvera choonadi ndipo zotsatira zake n’zakuti mumakonda abale mopanda chinyengo,+ kondanani kwambiri kuchokera mumtima.+