Yohane 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komabe onse amene anamulandira,+ anawapatsa mphamvu zokhala ana a Mulungu,+ chifukwa amenewa anakhulupirira m’dzina lake.+ Agalatiya 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zinatero kuti amasule anthu okhala pansi pa chilamulo mwa kuwagula,+ kutinso Mulungu atitenge ife kukhala ana ake.+
12 Komabe onse amene anamulandira,+ anawapatsa mphamvu zokhala ana a Mulungu,+ chifukwa amenewa anakhulupirira m’dzina lake.+
5 Zinatero kuti amasule anthu okhala pansi pa chilamulo mwa kuwagula,+ kutinso Mulungu atitenge ife kukhala ana ake.+