Aroma 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Monga mmene Malemba amanenera kuti: “Chifukwa cha inu, tikuphedwa nthawi zonse. Takhala ngati nkhosa zokaphedwa.”+ 1 Akorinto 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti ndikuona ngati Mulungu waika atumwife kukhala ngati omalizira pachionetsero+ monga anthu okaphedwa,+ chifukwa takhala ngati choonetsedwa m’bwalo la masewera+ kudziko, kwa angelo,+ ndi kwa anthu.+ 1 Akorinto 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsiku ndi tsiku ndimakhala pa ngozi yoti ndikhoza kufa.+ Ndikukutsimikizirani zimenezi ndili wokondwera nanu,+ abale, kukondwera kumene ndili nako mwa Khristu Yesu Ambuye wathu.
36 Monga mmene Malemba amanenera kuti: “Chifukwa cha inu, tikuphedwa nthawi zonse. Takhala ngati nkhosa zokaphedwa.”+
9 Pakuti ndikuona ngati Mulungu waika atumwife kukhala ngati omalizira pachionetsero+ monga anthu okaphedwa,+ chifukwa takhala ngati choonetsedwa m’bwalo la masewera+ kudziko, kwa angelo,+ ndi kwa anthu.+
31 Tsiku ndi tsiku ndimakhala pa ngozi yoti ndikhoza kufa.+ Ndikukutsimikizirani zimenezi ndili wokondwera nanu,+ abale, kukondwera kumene ndili nako mwa Khristu Yesu Ambuye wathu.