Aroma 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Motero tinaikidwa m’manda+ pamodzi ndi iye pobatizidwa mu imfa yake, kuti monga mmene Khristu anaukitsidwira kwa akufa mwa ulemerero wa Atate,+ ifenso tiziyenda m’moyo watsopano.+ 1 Akorinto 15:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Mmene wopangidwa ndi fumbiyo alili,+ ndi mmenenso opangidwa ndi fumbiwo alili. Ndipo mmene wakumwambayo alili,+ ndi mmenenso akumwambawo alili.+
4 Motero tinaikidwa m’manda+ pamodzi ndi iye pobatizidwa mu imfa yake, kuti monga mmene Khristu anaukitsidwira kwa akufa mwa ulemerero wa Atate,+ ifenso tiziyenda m’moyo watsopano.+
48 Mmene wopangidwa ndi fumbiyo alili,+ ndi mmenenso opangidwa ndi fumbiwo alili. Ndipo mmene wakumwambayo alili,+ ndi mmenenso akumwambawo alili.+