2 Akorinto 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndikanakonda kuti mundilole kuti ndidzikweze pang’ono.+ Ndipotu zoona zake n’zakuti, mwandilola kale. 2 Akorinto 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndikubwerezanso kunena kuti, munthu asandiyese wodzikweza. Koma ngati mukundionabe motero, ndilandirenibe monga wodzikweza yemweyo, kuti nanenso ndidzitame pang’ono.+
11 Ndikanakonda kuti mundilole kuti ndidzikweze pang’ono.+ Ndipotu zoona zake n’zakuti, mwandilola kale.
16 Ndikubwerezanso kunena kuti, munthu asandiyese wodzikweza. Koma ngati mukundionabe motero, ndilandirenibe monga wodzikweza yemweyo, kuti nanenso ndidzitame pang’ono.+