2 Akorinto 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tito ndinamuchonderera kuti abwere kwa inu ndipo ndinatumiza m’bale wina limodzi naye. Kodi Titoyo anakuchenjererani m’pang’ono pomwe ngati?+ Ayi ndithu sanatero. Tinayenda mumzimu umodzi,+ kodi si choncho? M’mapazi amodzimodzi, si choncho kodi?
18 Tito ndinamuchonderera kuti abwere kwa inu ndipo ndinatumiza m’bale wina limodzi naye. Kodi Titoyo anakuchenjererani m’pang’ono pomwe ngati?+ Ayi ndithu sanatero. Tinayenda mumzimu umodzi,+ kodi si choncho? M’mapazi amodzimodzi, si choncho kodi?