2 Akorinto 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zimenezi zinatichititsa kuti timulimbikitse Tito+ kuti, popeza iye ndiye anayambitsa zoperekazi pakati panu, iyeyo amalizitse kusonkhanitsa mphatso zanu zachifundo. 2 Akorinto 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tikuyamika Mulungu chifukwa Tito amakuderaninso nkhawa ngati mmene ifeyo timachitira,+
6 Zimenezi zinatichititsa kuti timulimbikitse Tito+ kuti, popeza iye ndiye anayambitsa zoperekazi pakati panu, iyeyo amalizitse kusonkhanitsa mphatso zanu zachifundo.