2 Akorinto 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti ndikudziwa kuti muli ndi mtima wofunitsitsa ndipo ndikunena zimenezi monyadira kwa Amakedoniya. Ndikumawauza kuti, “Abale a ku Akaya akhala okonzeka kwa chaka chimodzi tsopano,”+ ndipo kudzipereka kwanu kwalimbikitsa ambiri a iwo. 1 Timoteyo 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Uwalamule kuti azichita zabwino,+ akhale olemera pa ntchito zabwino,+ owolowa manja, okonzeka kugawira ena,+
2 Pakuti ndikudziwa kuti muli ndi mtima wofunitsitsa ndipo ndikunena zimenezi monyadira kwa Amakedoniya. Ndikumawauza kuti, “Abale a ku Akaya akhala okonzeka kwa chaka chimodzi tsopano,”+ ndipo kudzipereka kwanu kwalimbikitsa ambiri a iwo.
18 Uwalamule kuti azichita zabwino,+ akhale olemera pa ntchito zabwino,+ owolowa manja, okonzeka kugawira ena,+