2 Akorinto 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipereke maganizo anga pamenepa:+ nkhani imeneyi ndi yopindulitsa kwa inu,+ poona kuti chaka chimodzi chatha kale kuyambira pamene munayambitsa zimenezi. Sikuti munangoziyambitsa chabe, komanso munazichita modzipereka kwambiri.+
10 Ndipereke maganizo anga pamenepa:+ nkhani imeneyi ndi yopindulitsa kwa inu,+ poona kuti chaka chimodzi chatha kale kuyambira pamene munayambitsa zimenezi. Sikuti munangoziyambitsa chabe, komanso munazichita modzipereka kwambiri.+