2 Akorinto 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi tikuyambanso kudzichitira umboni tokha?+ Kapena kodi n’kofunika kuti ifenso, mofanana ndi anthu ena, tikhale ndi makalata+ otichitira umboni kwa inu kapena ochokera kwa inu? 2 Akorinto 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sikuti tayambanso kudzichitira umboni+ tokha kwa inu ayi, koma tikukupatsani chifukwa chodzitamandira, ndipo chifukwacho ndifeyo,+ kuti muwayankhe amene amadzitama chifukwa cha maonekedwe akunja,+ osati chifukwa cha mtima.+
3 Kodi tikuyambanso kudzichitira umboni tokha?+ Kapena kodi n’kofunika kuti ifenso, mofanana ndi anthu ena, tikhale ndi makalata+ otichitira umboni kwa inu kapena ochokera kwa inu?
12 Sikuti tayambanso kudzichitira umboni+ tokha kwa inu ayi, koma tikukupatsani chifukwa chodzitamandira, ndipo chifukwacho ndifeyo,+ kuti muwayankhe amene amadzitama chifukwa cha maonekedwe akunja,+ osati chifukwa cha mtima.+