2 Akorinto 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sikuti tayambanso kudzichitira umboni+ tokha kwa inu ayi, koma tikukupatsani chifukwa chodzitamandira, ndipo chifukwacho ndifeyo,+ kuti muwayankhe amene amadzitama chifukwa cha maonekedwe akunja,+ osati chifukwa cha mtima.+ 2 Akorinto 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti sitidzayesa n’komwe kudziona ngati ndife ofanana ndi anthu enaake kapena kudziyerekezera ndi ena amene amadzikweza.+ Ndithudi anthu amenewo samvetsa kanthu kalikonse chifukwa akuyezana okhaokha pogwiritsira ntchito miyezo yawo yomwe, ndipo akudziyerekezera ndi iwo eni.+
12 Sikuti tayambanso kudzichitira umboni+ tokha kwa inu ayi, koma tikukupatsani chifukwa chodzitamandira, ndipo chifukwacho ndifeyo,+ kuti muwayankhe amene amadzitama chifukwa cha maonekedwe akunja,+ osati chifukwa cha mtima.+
12 Pakuti sitidzayesa n’komwe kudziona ngati ndife ofanana ndi anthu enaake kapena kudziyerekezera ndi ena amene amadzikweza.+ Ndithudi anthu amenewo samvetsa kanthu kalikonse chifukwa akuyezana okhaokha pogwiritsira ntchito miyezo yawo yomwe, ndipo akudziyerekezera ndi iwo eni.+