Miyambo 25:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kudya uchi wambiri si bwino,+ ndipo anthu akamafunafuna okha ulemerero, kodi umenewo ndi ulemererodi?+ Miyambo 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi waona munthu wodziona ngati wanzeru m’maso mwake?+ Munthu wopusa ali ndi chiyembekezo chachikulu+ kuposa iyeyo. Agalatiya 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ngati wina akudziona kuti ndi wofunika pamene si wotero,+ akudzinyenga. Agalatiya 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma aliyense payekha ayese ntchito yake, kuti aone kuti ndi yotani.+ Akatero adzakhala ndi chifukwa chosangalalira ndi ntchito yake, osati modziyerekezera+ ndi munthu wina.
27 Kudya uchi wambiri si bwino,+ ndipo anthu akamafunafuna okha ulemerero, kodi umenewo ndi ulemererodi?+
12 Kodi waona munthu wodziona ngati wanzeru m’maso mwake?+ Munthu wopusa ali ndi chiyembekezo chachikulu+ kuposa iyeyo.
4 Koma aliyense payekha ayese ntchito yake, kuti aone kuti ndi yotani.+ Akatero adzakhala ndi chifukwa chosangalalira ndi ntchito yake, osati modziyerekezera+ ndi munthu wina.