1 Samueli 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano ufumu wako sukhalitsa.+ Yehova apeza munthu wapamtima pake,+ ndipo Yehova amuika kukhala mtsogoleri+ wa anthu ake chifukwa iwe sunasunge zimene Yehova anakulamula.”+ Miyambo 29:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anthu ambiri amafuna kuonana ndi mtsogoleri,+ koma chiweruzo cha munthu chimachokera kwa Yehova.+
14 Tsopano ufumu wako sukhalitsa.+ Yehova apeza munthu wapamtima pake,+ ndipo Yehova amuika kukhala mtsogoleri+ wa anthu ake chifukwa iwe sunasunge zimene Yehova anakulamula.”+