Ekisodo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Mose anauza Yehova kuti: “Pepani Yehova, ine sinditha kulankhula, kuyambira kalekale, kapena pamene mwalankhula ndi ine mtumiki wanu. Pakuti ndimalankhula movutikira ndipo ndine wa lilime lolemera.”+ 2 Akorinto 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti ena amati: “Makalata ake ndi olemerera ndi amphamvu, koma iyeyo akakhala pakati pathu amaoneka wofooka+ ndipo nkhani zake n’zosagwira mtima.”+
10 Ndiyeno Mose anauza Yehova kuti: “Pepani Yehova, ine sinditha kulankhula, kuyambira kalekale, kapena pamene mwalankhula ndi ine mtumiki wanu. Pakuti ndimalankhula movutikira ndipo ndine wa lilime lolemera.”+
10 Pakuti ena amati: “Makalata ake ndi olemerera ndi amphamvu, koma iyeyo akakhala pakati pathu amaoneka wofooka+ ndipo nkhani zake n’zosagwira mtima.”+