2 Akorinto 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti ngakhale nditati ndidzitamandire+ mopitirirako muyezo za ulamuliro umene Ambuye anatipatsa kuti tikulimbikitseni, osati kukupasulani,+ sindingachite manyazi. 2 Akorinto 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndikubwerezanso kunena kuti, munthu asandiyese wodzikweza. Koma ngati mukundionabe motero, ndilandirenibe monga wodzikweza yemweyo, kuti nanenso ndidzitame pang’ono.+
8 Pakuti ngakhale nditati ndidzitamandire+ mopitirirako muyezo za ulamuliro umene Ambuye anatipatsa kuti tikulimbikitseni, osati kukupasulani,+ sindingachite manyazi.
16 Ndikubwerezanso kunena kuti, munthu asandiyese wodzikweza. Koma ngati mukundionabe motero, ndilandirenibe monga wodzikweza yemweyo, kuti nanenso ndidzitame pang’ono.+