Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 8:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Poyankha iwo anati: “Atate wathu ndi Abulahamu.”+ Yesu anawauza kuti: “Ngati ndinu ana a Abulahamu,+ chitani ntchito za Abulahamu.

  • Aroma 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Chotero iye anapatsidwa lonjezolo+ chifukwa cha chikhulupiriro, kuti likhale mwa kukoma mtima kwakukulu,+ ndiponso kuti likhale lotsimikizika kwa mbewu yake yonse,+ osati yotsatira Chilamulo yokha ayi, komanso yotsatira chikhulupiriro cha Abulahamu. (Iye ndiye tate+ wa ife tonse,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena