Aroma 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kunena zoona,+ Khristu anakhaladi mtumiki+ kwa anthu odulidwa+ kuti atsimikizire kuti Mulungu ndi wokhulupirika. Komanso iye anasonyeza kuti malonjezo+ amene Mulunguyo anapatsa makolo awo ndi otsimikizirika, Agalatiya 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Malemba+ anatsekera zinthu zonse n’kuziika pansi pa uchimo,+ kuti lonjezolo, limene limakhalapo mwa kukhulupirira Yesu Khristu, liperekedwe kwa okhulupirirawo.+
8 Kunena zoona,+ Khristu anakhaladi mtumiki+ kwa anthu odulidwa+ kuti atsimikizire kuti Mulungu ndi wokhulupirika. Komanso iye anasonyeza kuti malonjezo+ amene Mulunguyo anapatsa makolo awo ndi otsimikizirika,
22 Koma Malemba+ anatsekera zinthu zonse n’kuziika pansi pa uchimo,+ kuti lonjezolo, limene limakhalapo mwa kukhulupirira Yesu Khristu, liperekedwe kwa okhulupirirawo.+