2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu+ akachimwa mosadziwa+ mwa kuchita zinthu zimene Yehova analamula kuti musachite, iye akachita chimodzi mwa zimenezo muzichita izi:
11 Ndiyeno ndifunse, Kodi anapunthwa mpaka kugweratu?+ Ayi! Koma chifukwa cha kulakwa kwawo+ pali chipulumutso kwa anthu a mitundu ina,+ kuti olakwawo achite nsanje.+