Machitidwe 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene anali kutumikira+ Yehova ndi kusala kudya, mzimu woyera unati: “Mwa anthu onse, mundipatulire Baranaba ndi Saulo+ kuti agwire ntchito imene ndinawaitanira.” Machitidwe 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pa chifukwa chimenechi, tonse tagwirizana chimodzi,+ ndipo tavomerezana kuti tisankhe amuna oti tiwatumize kwa inu limodzi ndi okondedwa athu, Baranaba ndi Paulo.+
2 Pamene anali kutumikira+ Yehova ndi kusala kudya, mzimu woyera unati: “Mwa anthu onse, mundipatulire Baranaba ndi Saulo+ kuti agwire ntchito imene ndinawaitanira.”
25 Pa chifukwa chimenechi, tonse tagwirizana chimodzi,+ ndipo tavomerezana kuti tisankhe amuna oti tiwatumize kwa inu limodzi ndi okondedwa athu, Baranaba ndi Paulo.+