Machitidwe 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo mawu aja anamvekanso kwa iye kachiwiri kuti: “Zinthu zimene Mulungu waziyeretsa usiyiretu kuzinena kuti n’zoipitsidwa.”+ Machitidwe 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo Petulo anayamba kulankhula kuti: “Ndazindikira ndithu kuti Mulungu alibe tsankho.+ Agalatiya 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Palibe Myuda kapena Mgiriki,+ palibe kapolo kapena mfulu,+ palibenso mwamuna kapena mkazi.+ Nonsenu ndinu munthu mmodzi mwa Khristu Yesu.+
15 Ndipo mawu aja anamvekanso kwa iye kachiwiri kuti: “Zinthu zimene Mulungu waziyeretsa usiyiretu kuzinena kuti n’zoipitsidwa.”+
28 Palibe Myuda kapena Mgiriki,+ palibe kapolo kapena mfulu,+ palibenso mwamuna kapena mkazi.+ Nonsenu ndinu munthu mmodzi mwa Khristu Yesu.+