Agalatiya 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tamverani! Ine Paulo, ndikukuuzani kuti mukadulidwa,+ Khristu sadzakhala waphindu kwa inu. Akolose 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anafafanizanso+ chikalata cholembedwa ndi manja,+ chokhala ndi malamulo+ operekedwa monga malangizo, chimene chinali kutitsutsa.+ Ndipo Iye wachichotsa mwa kuchikhomera+ pamtengo wozunzikirapo.*+
14 Anafafanizanso+ chikalata cholembedwa ndi manja,+ chokhala ndi malamulo+ operekedwa monga malangizo, chimene chinali kutitsutsa.+ Ndipo Iye wachichotsa mwa kuchikhomera+ pamtengo wozunzikirapo.*+