Yohane 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+ Aefeso 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Popeza maso+ a mtima wanu aunikiridwa,+ ndikukutchulanibe m’mapemphero anga kutinso mudziwe chiyembekezo+ chimene anakuitanirani, chuma chaulemerero+ chimene wasungira oyera monga cholowa,+
3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+
18 Popeza maso+ a mtima wanu aunikiridwa,+ ndikukutchulanibe m’mapemphero anga kutinso mudziwe chiyembekezo+ chimene anakuitanirani, chuma chaulemerero+ chimene wasungira oyera monga cholowa,+